Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ ndipo sadzawalira maliro+ kapena kuikidwa m’manda+ koma adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Iwo adzafa ndi lupanga ndiponso njala yaikulu.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.’+

  • Yeremiya 25:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pa tsiku limenelo padzakhala anthu ophedwa ndi Yehova kuchokera kumalekezero a dziko lapansi kufikanso kumalekezero ena a dziko lapansi.+ Sadzawalira maliro, kuwasonkhanitsa pamodzi, kapena kuwaika m’manda.+ Iwo adzakhala ngati manyowa panthaka.’+

  • Ezekieli 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mnofu wako ndidzauika m’mapiri, ndipo m’zigwa ndidzadzazamo zotsalira za mtembo wako.+

  • Yoweli 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndidzakuchotserani mdani wa kumpoto+ kuti akhale kutali ndi inu. Ndidzamuthamangitsira kudziko lopanda madzi ndi labwinja, nkhope yake itayang’ana kunyanja ya kum’mawa*+ ndipo nkhongo yake italoza kunyanja ya kumadzulo.*+ Fungo lake lonunkha lidzamveka ndipo fungo lake loipalo lidzapitirizabe kumveka+ pakuti Mulungu adzachita zinthu zazikulu.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena