Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 34:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa, ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera m’mwamba.+ Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.+

  • Yesaya 66:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+

  • Yeremiya 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu ofunkha adutsa m’njira zonse zodutsidwadutsidwa za m’chipululu. Lupanga la Yehova likuwononga anthu kuchokera kumalekezero a dziko kukafika kumalekezero ena a dziko.+ Palibe mtendere kwa munthu aliyense.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena