Ezekieli 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ine ndikubweretsera alendo,+ anthu ankhanza a mitundu ina.+ Iwo adzasolola lupanga n’kuwononga chilichonse chokongola chimene unapeza chifukwa cha nzeru zako, ndipo adzaipitsa ulemerero wako wonyezimira.+ Habakuku 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+
7 ine ndikubweretsera alendo,+ anthu ankhanza a mitundu ina.+ Iwo adzasolola lupanga n’kuwononga chilichonse chokongola chimene unapeza chifukwa cha nzeru zako, ndipo adzaipitsa ulemerero wako wonyezimira.+
6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+