Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+ Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Ezekieli 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+