16 “‘“Chifukwa cha kuchuluka kwa malonda ako,+ mwa iwe munadzaza zachiwawa ndipo unayamba kuchita machimo.+ Iwe kerubi amene umagwira ntchito yoteteza, ine ndidzakutulutsa m’phiri la Mulungu monga wodetsedwa ndipo ndidzakuwononga pakati pa miyala yamoto.+