Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Salimo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Ezekieli 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Lupanga la mfumu ya Babulo lidzafika pa iwe.+
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+
13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Ezekieli 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Lupanga la mfumu ya Babulo lidzafika pa iwe.+