Yesaya 62:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+ Ezekieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Umve mawu ochokera pakamwa panga ndipo undichenjezere anthuwo.+
6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+
17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Umve mawu ochokera pakamwa panga ndipo undichenjezere anthuwo.+