Yeremiya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+ Ezekieli 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yemwe ali kutali+ adzaphedwa ndi mliri. Yemwe ali pafupi adzaphedwa ndi lupanga. Yemwe watsala ali wotetezeka adzafa ndi njala, ndipo ukali wanga ndidzauthetsera pa iwo.+
12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+
12 Yemwe ali kutali+ adzaphedwa ndi mliri. Yemwe ali pafupi adzaphedwa ndi lupanga. Yemwe watsala ali wotetezeka adzafa ndi njala, ndipo ukali wanga ndidzauthetsera pa iwo.+