Yeremiya 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachititsa nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda kukhalanso ndi anthu ochuluka ndiponso ziweto zochuluka,” watero Yehova.+ Yeremiya 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+
27 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachititsa nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda kukhalanso ndi anthu ochuluka ndiponso ziweto zochuluka,” watero Yehova.+
12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+