Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Salimo 104:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mukatumiza mzimu wanu zimalengedwa.+Ndipo mumachititsa dziko kukhala latsopano. Ezekieli 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Ndidzaika mzimu wanga mwa inu ndipo mudzakhala amoyo.+ Ndidzakukhazikani m’dziko lanu ndipo mudzadziwa kuti ine Yehova ndinanena zimenezi ndipo ndazichita,’ watero Yehova.”+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
14 ‘Ndidzaika mzimu wanga mwa inu ndipo mudzakhala amoyo.+ Ndidzakukhazikani m’dziko lanu ndipo mudzadziwa kuti ine Yehova ndinanena zimenezi ndipo ndazichita,’ watero Yehova.”+