Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+ Ezekieli 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzakhala m’dzikolo popanda chowaopseza,+ adzamanga nyumba+ ndi kulima minda ya mpesa.+ Iwo adzakhala mwabata+ ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene akuwatonza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’” Ezekieli 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+
6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+
26 Adzakhala m’dzikolo popanda chowaopseza,+ adzamanga nyumba+ ndi kulima minda ya mpesa.+ Iwo adzakhala mwabata+ ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene akuwatonza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”
25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+