Zekariya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene adzamenyane ndi Yerusalemu ndi uwu:+ Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire,+ maso ake adzawola ali m’malo mwake ndiponso lilime lake lidzawola m’kamwa mwake.
12 “Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene adzamenyane ndi Yerusalemu ndi uwu:+ Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire,+ maso ake adzawola ali m’malo mwake ndiponso lilime lake lidzawola m’kamwa mwake.