Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+

  • Salimo 110:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova amene ali kudzanja lako lamanja+

      Adzaphwanyaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wake.+

  • Yoweli 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ine ndidzasonkhanitsanso pamodzi mitundu yonse ya anthu+ ndi kuibweretsa m’chigwa cha Yehosafati+ ndipo ndidzaiweruza chifukwa cha anthu anga ndi cholowa changa, Isiraeli.+ Mitundu imeneyi inamwaza Isiraeli pakati pa mitundu ya anthu ndiponso inagawana dziko langa.+

  • Mika 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Tsopano mitundu yambiri ya anthu idzasonkhana kuti ikuukire. Mitunduyo ikunena kuti, ‘Tiyeni timuwononge ndipo maso athu aone kuwonongeka kwa Ziyoni.’+

  • Chivumbulutso 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena