Yesaya 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+ Ezekieli 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzamuweruza+ ndi mliri+ ndiponso magazi.+ Ndidzamugwetsera mvula yamphamvu, matalala,+ moto+ ndi sulufule. Ndidzagwetsa zimenezi pa iyeyo, pagulu lake la asilikali ndi pa mitundu yambiri ya anthu amene adzakhale kumbali yake.+
16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+
22 Ine ndidzamuweruza+ ndi mliri+ ndiponso magazi.+ Ndidzamugwetsera mvula yamphamvu, matalala,+ moto+ ndi sulufule. Ndidzagwetsa zimenezi pa iyeyo, pagulu lake la asilikali ndi pa mitundu yambiri ya anthu amene adzakhale kumbali yake.+