Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo + amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula pamalo awo.+ Ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.+

  • Ezekieli 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Iwe unanena kuti, ‘Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi mayiko awiri awa zidzakhala zanga ndipo ife tidzatenga mayiko awiri onsewo.’+ Unanena zimenezi ngakhale kuti Yehova anali komweko.+

  • Zefaniya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ndamva chitonzo cha Mowabu+ ndi mawu onyoza a ana a Amoni+ amene anali kunena kwa anthu anga. Iwo anali kuopseza anthu anga modzitukumula kuti awalanda dziko lawo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena