Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+ Ezekieli 48:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Kuzungulira mzindawo pakhale mtunda wokwana mikono 18,000. Kuyambira pa tsiku limenelo, dzina la mzindawo lidzakhala lakuti, Yehova Ali Kumeneko.”+ Zefaniya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wachotsa zigamulo zake pa iwe.+ Watembenuza ndi kubweza mdani wako.+ Mfumu ya Isiraeli, Yehova, ali pakati pa anthu ako+ ndipo sudzaopanso kuti tsoka likugwera.+
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
35 “Kuzungulira mzindawo pakhale mtunda wokwana mikono 18,000. Kuyambira pa tsiku limenelo, dzina la mzindawo lidzakhala lakuti, Yehova Ali Kumeneko.”+
15 Yehova wachotsa zigamulo zake pa iwe.+ Watembenuza ndi kubweza mdani wako.+ Mfumu ya Isiraeli, Yehova, ali pakati pa anthu ako+ ndipo sudzaopanso kuti tsoka likugwera.+