Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zefaniya 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Choncho pitirizani kundiyembekezera,’+ watero Yehova, ‘mpaka tsiku limene ndidzanyamuka kuti ndikaukire ndi kulanda zinthu zofunkhidwa.+ Chigamulo changa ndicho kusonkhanitsa mitundu ya anthu+ ndi kusonkhanitsa pamodzi maufumu kuti ndiwadzudzule mwamphamvu+ ndi kuwatsanulira mkwiyo wanga wonse woyaka moto, pakuti moto wa mkwiyo wanga udzanyeketsa dziko lonse lapansi.+

  • Zekariya 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndidzasonkhanitsa mitundu yonse ya anthu kuti imenyane ndi Yerusalemu.+ Mzindawu udzalandidwa,+ katundu wa m’nyumba adzatengedwa ndipo akazi adzagwiriridwa.+ Hafu ya anthu a mumzindawu idzatengedwa kupita kudziko lina,+ koma anthu otsala+ sadzachotsedwa mumzindawu.+

  • Chivumbulutso 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo anawasonkhanitsa pamodzi, kumalo amene m’Chiheberi amatchedwa Haramagedo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena