1 Mafumu 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khonde+ la kutsogolo kwa chipinda chachikulu* cha nyumbayo linali mikono 20 m’litali, kufanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo, ndipo linali mikono 10 m’lifupi mwake. 2 Mbiri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kutsata m’litali mwa nyumbayo, kumaso kwake kunali khonde+ la mikono 20 m’litali, mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 120, ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.
3 Khonde+ la kutsogolo kwa chipinda chachikulu* cha nyumbayo linali mikono 20 m’litali, kufanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo, ndipo linali mikono 10 m’lifupi mwake.
4 Kutsata m’litali mwa nyumbayo, kumaso kwake kunali khonde+ la mikono 20 m’litali, mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 120, ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.