-
Ezekieli 41:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kumadzulo kwa nyumbayo kunalinso nyumba ina. Nyumba imeneyo inali mikono 70 m’lifupi mwake. Khoma lonse la nyumbayo linali lochindikala mikono isanu, ndipo m’litali mwake linali mikono 90. Pakati pa nyumba ziwirizi panali mpata waukulu.
-