2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600. Ezekieli 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anayeza makoma a chipinda chamkati kumbuyo kwa kachisi, ndipo anapeza kuti anali mikono 20 m’litali ndi mikono 20 m’lifupi.+ Kenako anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+
8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.
4 Ndiyeno anayeza makoma a chipinda chamkati kumbuyo kwa kachisi, ndipo anapeza kuti anali mikono 20 m’litali ndi mikono 20 m’lifupi.+ Kenako anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+