Yeremiya 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi pamapiri. Katundu wanu ndi chuma chanu chonse ndidzazipereka kuti anthu azifunkhe.+ Ndidzapereka malo anu okwezeka chifukwa cha tchimo limene lachitika m’madera anu onse.+ Ezekieli 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzakupereka m’manja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzafafaniza mulu wako wadothi+ ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zokongola+ n’kukusiya wosavala ndi wamaliseche.
3 ndi pamapiri. Katundu wanu ndi chuma chanu chonse ndidzazipereka kuti anthu azifunkhe.+ Ndidzapereka malo anu okwezeka chifukwa cha tchimo limene lachitika m’madera anu onse.+
39 Ndidzakupereka m’manja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzafafaniza mulu wako wadothi+ ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zokongola+ n’kukusiya wosavala ndi wamaliseche.