Ezekieli 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Munthu uja ananditengera+ kubwalo lakunja kudzera mbali ya kumpoto.+ Kumeneko anandipititsa kumdadada wa zipinda zodyeramo+ zimene zinali kutsogolo kwa mpata waukulu,+ ndiponso kumpoto kwa nyumba imene inali kumadzulo.
42 Munthu uja ananditengera+ kubwalo lakunja kudzera mbali ya kumpoto.+ Kumeneko anandipititsa kumdadada wa zipinda zodyeramo+ zimene zinali kutsogolo kwa mpata waukulu,+ ndiponso kumpoto kwa nyumba imene inali kumadzulo.