Yesaya 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+
8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+