63 Ndidzachita izi kuti ndikadzakuperekera nsembe yophimba machimo+ chifukwa cha zonse zimene wachita, udzakumbukire ndi kuchita manyazi+ ndiponso kuti usadzakhale ndi chifukwa chilichonse chotsegulira pakamwa pako+ chifukwa cha manyazi ako,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”