Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Monga mmene kum’mawa kwatalikirana ndi kumadzulo,+Momwemonso, watiikira kutali zolakwa zathu.+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+