-
Ezekieli 46:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Popereka ng’ombe yaing’ono yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa. Popereka nkhosa yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa. Popereka ana a nkhosa amphongo aziperekanso nsembe yambewu imene angakwanitse. Pa nsembe iliyonse yambewu yokwana muyezo wa efa, azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+
-