-
Oweruza 10:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho, amenewa anazunza ndi kupondereza kwambiri ana a Isiraeli chaka chimenecho. Kwa zaka 18, anapondereza ana onse a Isiraeli amene anali kum’mawa kwa Yorodano, m’dziko la Aamori limene linali ku Giliyadi.
-