Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 48:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, ndi ana anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga monga alili Rubeni ndi Simiyoni.+

  • Yoswa 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+

  • Yoswa 17:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Poyankha, Yoswa anauza anthu a fuko la Yosefe, omwe ndi Efuraimu ndi Manase, kuti: “Ndinu anthu ochuluka, ndipo ndinu amphamvu kwambiri.+ Simuyenera kukhala ndi gawo limodzi lokha,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena