-
Ezekieli 45:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “‘Malo a mtsogoleri wa anthu adzakhale kumbali iyi ndi kumbali ina ya chopereka chopatulika+ ndi ya malo a mzinda. Adzakhale pafupi ndi chopereka chopatulika komanso pafupi ndi malo a mzindawo. Malo a mtsogoleriwo adzakhale kumadzulo ndi kum’mawa. M’litali mwake adzakhale ofanana ndi magawo a malo amene mafuko a Isiraeli adzalandire, kuchokera kumalire a kumadzulo kukafika kumalire a kum’mawa.+
-