Salimo 45:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana anu adzatenga+ malo a makolo anu,+Ndipo mudzawaika kukhala akalonga padziko lonse lapansi.+ Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo.