Yeremiya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.” Ezekieli 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira.+ Choncho ine ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi, n’kufuula+ kuti: “Kalanga ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa!+ Kodi mukufuna kufafaniziratu Aisiraeli otsalawa?”+
10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”
13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira.+ Choncho ine ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi, n’kufuula+ kuti: “Kalanga ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa!+ Kodi mukufuna kufafaniziratu Aisiraeli otsalawa?”+