Ezekieli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+
16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+