Salimo 137:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Tinakhala pansi+ m’mphepete mwa mitsinje ya ku Babulo,+Ndipo tinalira titakumbukira Ziyoni.+