Numeri 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma Mose anati: “N’chifukwa chiyani mukuphwanya lamulo la Yehova?+ Zimenezo sizikuthandizani. 2 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Taonani, ife patsogolo pathu pali Mulungu woona+ ndi ansembe ake,+ ndi malipenga+ otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu,+ chifukwa simupambana.”+ Yeremiya 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ukuloseranso kuti, ‘Mfumu ya Babulo idzatenga Zedekiya kupita naye ku Babulo ndipo adzakhala komweko kufikira nditamucheukira,’+ watero Yehova. Ukunenanso kuti, ‘ngakhale kuti anthu inu mukupitiriza kumenyana ndi Akasidi simudzapambana.’ N’chifukwa chiyani ukulosera zimenezi?”+
12 Taonani, ife patsogolo pathu pali Mulungu woona+ ndi ansembe ake,+ ndi malipenga+ otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu,+ chifukwa simupambana.”+
5 Ukuloseranso kuti, ‘Mfumu ya Babulo idzatenga Zedekiya kupita naye ku Babulo ndipo adzakhala komweko kufikira nditamucheukira,’+ watero Yehova. Ukunenanso kuti, ‘ngakhale kuti anthu inu mukupitiriza kumenyana ndi Akasidi simudzapambana.’ N’chifukwa chiyani ukulosera zimenezi?”+