Ezekieli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi. Idya mpukutuwu,+ kenako upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.” Chivumbulutso 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, mawu+ amene ndinawamva kuchokera kumwamba aja, analankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wofunyulula umene uli m’dzanja la mngelo amene waimirira panyanja ndi pamtunda uja.”+
3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi. Idya mpukutuwu,+ kenako upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.”
8 Kenako, mawu+ amene ndinawamva kuchokera kumwamba aja, analankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wofunyulula umene uli m’dzanja la mngelo amene waimirira panyanja ndi pamtunda uja.”+