1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+ Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+