Ezekieli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzamutambasulira ukonde wanga. Chotero iye adzakodwa mu ukonde wanga wosakira+ ndipo ndidzamupititsa ku Babulo, kudziko la Akasidi.+ Koma iye sadzaliona ndipo adzafera komweko.+ Ezekieli 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzam’ponyera ukonde wanga ndipo adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Ndiyeno ndidzamubweretsa ku Babulo ndi kumuweruza chifukwa chondichitira zinthu mosakhulupirika.+
13 Ine ndidzamutambasulira ukonde wanga. Chotero iye adzakodwa mu ukonde wanga wosakira+ ndipo ndidzamupititsa ku Babulo, kudziko la Akasidi.+ Koma iye sadzaliona ndipo adzafera komweko.+
20 Ndidzam’ponyera ukonde wanga ndipo adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Ndiyeno ndidzamubweretsa ku Babulo ndi kumuweruza chifukwa chondichitira zinthu mosakhulupirika.+