Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+

  • Yeremiya 34:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iweyo sudzazemba kuti asakugwire chifukwa adzakugwira ndithu ndi kukupereka m’manja mwake.+ Udzaonana ndi mfumu ya Babulo+ maso ndi maso, ndipo idzalankhula nawe ndi kupita nawe ku Babulo.’

  • Yeremiya 39:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu maso a Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga m’maunyolo amkuwa kuti apite naye ku Babulo.

  • Yeremiya 52:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga ndi maunyolo amkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Kumeneko anamuika m’ndende mpaka tsiku la imfa yake.

  • Ezekieli 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, “Pali ine Mulungu wamoyo,+ munthu amene ananyoza lumbiro+ ndi kuphwanya pangano limene anachita ndi mfumu imene inamulonga ufumu, adzafera m’dziko la mfumu yomweyo, dziko la Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena