Yeremiya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ine lero ndakusandutsa mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri, mzati wachitsulo ndi makoma amkuwa+ kuti dziko lonseli lisakugonjetse.+ Ndithu kuti mafumu a Yuda, akalonga ake, ansembe ake ndi anthu a m’dzikoli asakugonjetse.+
18 Koma ine lero ndakusandutsa mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri, mzati wachitsulo ndi makoma amkuwa+ kuti dziko lonseli lisakugonjetse.+ Ndithu kuti mafumu a Yuda, akalonga ake, ansembe ake ndi anthu a m’dzikoli asakugonjetse.+