Yobu 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+ Salimo 107:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mulungu akutsanulira mnyozo pa anthu olemekezeka,+Moti iye akuwachititsa kuyendayenda m’chipululu, mmene mulibe njira.+
19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+
40 Mulungu akutsanulira mnyozo pa anthu olemekezeka,+Moti iye akuwachititsa kuyendayenda m’chipululu, mmene mulibe njira.+