Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mlondayo anali kulankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo dulani nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndi kumwaza zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake,+

  • Danieli 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye anathamangitsidwa pakati pa anthu ndipo mtima wake unasinthidwa n’kukhala ngati wa nyama. Anayamba kukhala limodzi ndi abulu akutchire+ ndipo anali kudya udzu ngati ng’ombe. Thupi lake linkanyowa ndi mame akumwamba,+ kufikira pamene anadziwa kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu, ndiponso kuti akafuna kuika munthu aliyense kuti akhale wolamulira, amamuika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena