Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma mukandiuza malotowo ndi kuwamasulira, ine ndikupatsani mphatso, mphoto ndi ulemerero wochuluka.+ Choncho ndiuzeni malotowo ndipo muwamasulire.”

  • Danieli 2:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.

  • Danieli 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anaikanso nduna zapamwamba zitatu zoyang’anira masatarapiwo, ndipo Danieli anali mmodzi wa ndunazo.+ Anaika nduna zimenezi kuti nthawi zonse masatarapiwo+ aziziuza chilichonse chimene chikuchitika, ndi cholinga chakuti zinthu za mfumu zisawonongeke.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena