Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Muonetsetse kuti musanyalanyaze kuchita zimenezi kuti vuto limeneli lingakule, zomwe zingapweteketse mafumu.”+

  • Esitere 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa+ kuti tiwonongedwe, tiphedwe ndi kufafanizidwa.+ Ngati tikanagulitsidwa kukhala akapolo aamuna+ ndi akapolo aakazi ndikanakhala chete. Koma musalole kuti tsoka limeneli lichitike chifukwa liwonongetsa zinthu zambiri za mfumu.”

  • Luka 19:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Nangano n’chifukwa chiyani sunasungitse ndalama yanga yasilivayo kwa osunga ndalama? Ukanatero, ine pobwera ndikanaitenga limodzi ndi chiwongoladzanja chake.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena