-
Esitere 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno anapatsa Hataki kalata+ imene munali lamulo lochokera ku Susani+ lakuti Ayuda afafanizidwe. Anamupatsa kalata imeneyi kuti akaonetse Esitere ndi kumuuza+ kuti akaonekere kwa mfumu ndi kuipempha kuti iwakomere mtima,+ ndiponso kuti Esitere akachonderere mfumu mwachindunji m’malo mwa anthu a mtundu wake.+
-