Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tiyeni timugulitse kwa Aisimaeliwa,+ tisam’pweteke ayi.+ Ndipotu ndi m’bale wathu ameneyu, magazi* athu enieni.” Atamva mawuwa, iwo anamvera m’bale wawoyo.+

  • Nehemiya 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komatu ife ndi anzathuwo ndife pachibale.+ Ana athu aamuna n’chimodzimodzi ndi ana awo aamuna, koma ife tikusandutsa ana athu aamuna ndi ana athu aakazi kukhala akapolo.+ Ndipotu ena mwa ana athu aakazi tawasandutsa kale akapolo. Ife tilibenso mphamvu, chifukwa minda yathu ya tirigu ndi minda yathu ya mpesa ili m’manja mwa anthu ena.”

  • Yoweli 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 mwagulitsa ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu+ kwa ana a Agiriki,+ ndi cholinga choti muwachotse ndi kuwapititsa kutali ndi dziko lawo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena