Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 8:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kenako tinapereka malamulo+ a mfumu kwa masatarapi*+ a mfumu ndi abwanamkubwa+ a kutsidya lina la Mtsinje.*+ Iwo anathandiza anthuwo+ ndiponso anathandiza panyumba ya Mulungu woona.

  • Esitere 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho anaitana alembi+ a mfumu pa nthawi imeneyo, m’mwezi wachitatu umene ndi mwezi wa Sivani,* pa tsiku la 23 la mweziwo. Iwo analemba makalatawo mogwirizana ndi zimene Moredekai ananena. Makalatawo anali opita kwa Ayuda, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi akalonga a m’zigawo zonse kuchokera ku Indiya kukafika ku Itiyopiya, zigawo 127.+ Chigawo chilichonse anachilembera makalata amenewa malinga ndi mmene anthu a m’chigawocho anali kulembera+ ndiponso m’chinenero chawo.+ Nawonso Ayuda anawalembera malinga ndi mmene iwo anali kulembera ndiponso m’chinenero chawo.+

  • Danieli 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Nebukadinezara monga mfumu anatumiza uthenga kwa masatarapi,* akuluakulu a boma,*+ abwanamkubwa, alangizi, asungichuma, oweruza, akuluakulu apolisi+ ndi oyang’anira onse a zigawo kuti asonkhane ku mwambo wotsegulira+ fano limene mfumu Nebukadinezara inaimika.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena