Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Miyambo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wopanda chilungamo amakhala wonyansa kwa anthu olungama,+ ndipo munthu wowongoka m’njira yake amakhala wonyansa kwa munthu woipa.+ Mlaliki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.
27 Munthu wopanda chilungamo amakhala wonyansa kwa anthu olungama,+ ndipo munthu wowongoka m’njira yake amakhala wonyansa kwa munthu woipa.+
4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.