Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ Mateyu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso ndikukuuzani kuti, ngati awiri mwa inu padziko lapansi pano adzagwirizana pa chilichonse chofunika kupempha, Atate wanga wakumwamba adzawachitira.+
19 Ndiponso ndikukuuzani kuti, ngati awiri mwa inu padziko lapansi pano adzagwirizana pa chilichonse chofunika kupempha, Atate wanga wakumwamba adzawachitira.+