Genesis 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+ Malaki 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+
18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+