Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Danieli 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene unali kuyamba kupemphera ndinalandira uthenga, choncho ndabwera kudzakufotokozera za uthengawo chifukwa iwe ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.+ Tsopano khala tcheru,+ ndipo umvetsetse zinthu zimene ukuona.
23 Pamene unali kuyamba kupemphera ndinalandira uthenga, choncho ndabwera kudzakufotokozera za uthengawo chifukwa iwe ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.+ Tsopano khala tcheru,+ ndipo umvetsetse zinthu zimene ukuona.